Job 33:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati mngeloyo amkomera mtima, nati, ‘Mpulumutseni kuti asapite ku manda, dipo lake nali,’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo Mulungu amchitira chifundo, nati, Mlanditse, angatsikire kumanda, Ndampezera dipo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kudzamukomera mtima ndi kunena kuti, ‘Mupulumutseni kuti asapite ku manda; ine ndapeza cholowa mʼmalo mwa moyo wake,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Mulungu amcitira cifundo, nati, Mlanditse, angatsikire kumanda, Ndampezera dipo.