Job 33:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamenepo thupi lake lisanduke lasee ngati lapaubwana, ndipo iye abwerere ku masiku a unyamata wake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mnofu wake udzakhala see, woposa wa mwana; adzabwerera kumasiku a ubwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepo thupi lake lidzasanduka lasee ngati la mwana; ndipo adzabwezeretsedwanso kukhala ngati mʼmasiku a unyamata wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mnofu wace udzakhala se, woposa wa mwana; Adzabwerera ku masiku a ubwana wace.