Job 33:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo adzavomera pamaso pa anthu kuti, ‘Ndidachimwa, sindidachite zolungama. Koma Mulungu sadandilange koyenerana ndi kuchimwa kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apenyerera anthu, ndi kuti, ndinachimwa, ndaipsa choongokacho, ndipo sindinapindula nako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo adzabwera kwa anzake ndi kunena kuti, ‘Ndinachimwa ndipo sindinachite zolungama, koma sindinalangidwe koyenerana ndi kuchimwa kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apenyerera anthu, ndi kuti, Ndinacimwa, ndaipsa coongokaco, Ndipo sindinapindula nako.