Job 33:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena zoona, ine ndine mnzanu pamaso pa Mulungu, poti inenso adandiwumba ndi dothi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndikhala kwa Mulungu ngati inu; inenso ndinaumbidwa ndi dothi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndili monga inu pamaso pa Mulungu; nanenso ndinachokera ku dothi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndikhala kwa Mulungu ngati inu; Inenso ndinaumbidwa ndi dothi,