Job 33:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musachite mantha ndi kuwopsedwa nane, chifukwa sindikupanikizani koopsa ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, kuopsa kwanga simudzachita nako mantha; ndi ichi ndikusenzetsani sichidzakulemererani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musachite mantha ndipo musandiope ayi, Ine sindikupanikizani kwambiri ayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, kuopsa kwanga simudzacita nako mantha; Ndi ici ndikusenzetsani sicidzakulemererani.