Job 35:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena amaitana Mulungu koma Iye saŵayankha, chifukwa cha kunyada ndi kuipa kwa anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apo afuula, koma Iye sawayankha; chifukwa cha kudzikuza kwa anthu oipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye sayankha pamene anthu akufuwulira kwa Iye chifukwa cha kudzikuza kwa anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apo apfuula, koma Iye sawayankha; Cifukwa ca kudzikuza kwa anthu oipa.