Job 35:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu aYobe, mukunena kuti simungathe kupenya Mulungu, komabe mlandu wanu adzauzenga ndiye, ndipo mukudikira kuti augamule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde mungakhale munena, Sindimpenya, mlanduwo uli pamaso pake, ndipo mumlindira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndi bodza lalikulu kunena kuti Iye saona zimene zikuchitika. Iye adzaweruza molungama ngati inu mutamudikira
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde mungakhale munena, Sindimpenya, Mlanduwo uli pamaso pace, ndipo mumlindira.