Job 35:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapena kufunsa kuti, ‘Kodi kuchimwa kwanga ubwino wake ndi wotani? Nanga ndikadapindulanji ndikadaleka kuchimwa?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti munena, Upindulanji nacho? Posachimwa ndinapindula chiyani chimene sindikadapindula pochimwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso inu mukufunsa kuti, ‘Kodi phindu langa nʼchiyani, ndipo ndimapeza chiyani ndikapanda kuchimwa?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munena, Upindulanji naco? Posacimwa ndinapindula ciani cimene sindikadapindula pocimwa?