Job 35:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mukamachimwa, ndiye kuti mukumchita Mulungu chiyani? Mukamachulukitsa machimo anu, kodi mumamvuta bwanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mwachimwa, mumchitira Iye chiyani? Zikachuluka zolakwa zanu, mumchitira Iye chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inuyo mukachimwa, Iye zimamukhudza motani? Ngati machimo anu ndi ochuluka, zimenezo zimachita chiyani kwa Iye?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mwacimwa, mumcitira Iye ciani? Zikacuruka zolakwa zanu, mumcitira Iye ciani?