Job 35:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mukati ndinu wosalakwa, ndiye kuti mukumpindulira chiyani? Kodi angathe kulandiranji kwa inu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukakhala wolungama, mumninkhapo chiyani? Kapena alandira chiyani pa dzanja lanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati inu ndinu wolungama, mumamupatsa Iyeyo chiyani? Kapena Iye amalandira chiyani chochokera mʼdzanja lanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukakhala wolungama, mumninkhapo ciani? Kapena alandira ciani pa dzanja lanu?