Job 35:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuipa kwanu kumangovuta anthu anzanu, chimodzimodzinso ntchito zanu zabwino zimangopindulira anzanu basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Choipa chanu chikhoza kuipira munthu wonga inu, ndi chilungamo chanu chikhoza kukomera wobadwa ndi munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyipa kwanu kumangokhudza anthu ngati inuyo, ndipo chilungamo chanu chimakhudza anthu anzanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Coipa canu cikhoza kuipira munthu wonga inu, Ndi cilungamo canu cikhoza kukomera wobadwa ndi munthu.