Job 35:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu akufuula chifukwa cha kuzunzidwa. Akupempha chithandizo chifukwa anthu amphamvu akuŵavula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha kuchuluka masautso anthu anafuula, afuula chifukwa cha dzanja la amphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu akufuwula chifukwa cha kuzunzidwa; akufuna chithandizo kuti achoke pansi pa ulamuliro wa anthu amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca kucuruka masautso anthu anapfuula, Apfuula cifukwa ca dzanja la amphamvu.