Job 36:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati anthu amumvera ndi kumamtumikira, adzatsiriza masiku a moyo wao mwamtendere, adzatsiriza zaka zao mosangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akamvera ndi kumtumikira, adzatsiriza masiku ao modala, ndi zaka zao mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati iwo amumvera ndi kumutumikira, adzatsiriza masiku a moyo wawo mwamtendere, adzatsiriza zaka zawo mosangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akamvera ndi kumtumikira, Adzatsiriza masiku ao modala, Ndi zaka zao mokondwera.