Job 36:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akapanda kumvera, adzaonongeka ndi lupanga, adzafa osadziŵa kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akapanda kumvera adzatayika ndi lupanga, nadzatsirizika osadziwa kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati samvera, adzaphedwa ndi lupanga ndipo adzafa osadziwa kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akapanda kumvera adzatayika ndi lupanga, Nadzatsirizika osadziwa kanthu.