Job 36:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu onyoza Mulungu mumtima mwao amaputa mkwiyo wake, Mulungu akaŵalanga, iwo safuula kupempha chithandizo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo a mtima wakunyoza Mulungu, akundika mkwiyo, akawamanga Iye, safuulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu osapembedza amasunga mkwiyo mu mtima mwawo; akawalanga, safuwulira kwa Iye kupempha thandizo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo a mtima wakunyoza Mulungu, akundika mkwiyo, Akawamanga Iye, sapfuulira.