Job 36:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amafa akali biriŵiri, ndipo moyo wao umathera m'zonyansa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwowa akufa akali biriwiri, ndi moyo wao utayika ngati odetsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amafa akanali achinyamata, pakati pa amuna achiwerewere a kumalo azipembedzo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwowa akufa akali biriwiri, Ndi moyo wao utayika ngati odetsedwa.