Job 36:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu amapulumutsa ovutika mwa njira ya mazunzo ao omwe, amaŵatsekula makutu poŵagwetsa m'mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apulumutsa wozunzika mwa kuzunzika kwake, nawatsegulira m'khutu mwao mwa kupsinjika kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ovutika, Iye amawapulumutsa pa mavuto awo; Mulungu amawayankhula mʼmasautso awowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apulumutsa wozunzika mwa kuzunzika kwace, Nawatsegulira m'khutu mwao mwa kupsinjika kwao.