Job 36:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma tsopano inu mwapezeka opalamula ngati anthu oipa, choncho chilango cholungama cha Mulungu chakugwerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukadzazidwa nazo zolingirira oipa, zolingirirazo ndi chiweruzo zidzakugwiranibe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano inu mwapezeka wopalamula chifukwa cha kuyipa kwanu; chiweruzo ndi chilungamo chakugwerani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukadzazidwa nazo zolingirira oipa, Zolingirirazo ndi ciweruzo zidzakugwiranibe,