Job 36:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalakelake kuti usiku ubwere, chifukwa ndiyo nthaŵi imene mitundu ya anthu idzaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musakhumbe usiku, umene anthu alikhidwe m'malo mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalakalake kuti usiku ubwere, pakuti ndiyo nthawi imene anthu adzawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musakhumbe usiku, Umene anthu alikhidwe m'malo mwao.