Job 36:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, Mulungu ndi wamkulu ndiponso ndi wamphamvu. Kodi ndi mphunzitsi uti amene angafanane naye?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Mulungu achita mokwezeka mu mphamvu yake, mphunzitsi wakunga Iye ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Taonani, Mulungu ndi wamkulu ndiponso ndi wamphamvu. Kodi ndi mphunzitsi uti amene angafanane naye?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Mulungu acita mokwezeka mu mphamvu yace, Mphunzitsi wakunga Iye ndani?