Job 36:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe ndi mmodzi yemwe angauze Mulungu zoti achite. Palibe aliyense amene anganene kuti ‘Mulungu ndi wolakwa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamuikira njira yake ndani? Adzati ndani, Mwachita chosalungama?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani amene anamuwuzapo Mulungu zoti achite, kapena kumuwuza kuti, ‘Inu mwachita chinthu cholakwa?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamuikira njira yace ndani? Adzati ndani, Mwacita cosalungama?