Job 36:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kumbukirani kutamanda ntchito za Mulungu, zimene anthu amaziyamika ndi nyimbo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani kuti mukuze ntchito zake zimene anaziimbira anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani kutamanda ntchito zake zimene anthu amaziyamika mʼnyimbo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani kuti mukuze nchito zace, Zimene anaziyimbira anthu.