Job 36:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndiye amakweza timadontho ta madzi ku thambo kuchokera pansi, ndipo amasungunula mitambo kuti ikhale mvula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti akweza madontho a mvula, akhetsa mvula ya m'nkhungu yake
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mulungu ndiye amakweza timadontho tamadzi kuthambo, timene timasungunuka nʼkukhala mvula;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti akweza madontho a mvula, Akhetsa mvula ya m'nkhungu yace