Job 36:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi alipo wina woti angadziŵe kuyenda kwa mitambo kapena kugunda kwa zing'aning'ani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pali munthu kodi wodziwitsa mayalidwe a mitambo, ndi kugunda kwa msasa wake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani amene angadziwe momwe mitambo imayendera, momwe Iye amabangulira kuchokera kumalo ake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pali munthu kodi wodziwitsa mayalidwe a mitambo, Ndi kugunda kwa msasa wace?