Job 36:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nzeru zanga zikhala zochokera patali, ndiwonetsa kulungama kwa Mlengi wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzatenga nzeru zanga kutali, ndidzavomereza kuti Mlengi wanga ndi wolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nzeru zanga ndimazitenga kutali; ndidzaonetsa kulungama kwa Mlengi wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzatenga nzeru zanga kutali, Ndidzabvomereza kuti Mlengi wanga ndi wolungama.