Job 36:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amaŵalitsa zing'aning'ani kuthambo kwake konse, zimafika ngakhale pansi pa nyanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Iye ayala kuunika kwake pamenepo. Navundikira kunsi kwake kwa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani momwe amawalitsira zingʼaningʼani pa malo ake onse, zimafika ngakhale pansi pa nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Iye ayala kuunika kwace pamenepo. Nabvundikira kunsi kwace kwa nyanja.