Job 36:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amachenjeza mitundu ya anthu podzera m'zimenezi, komabe amapereka chakudya chochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti aweruza nazo mitundu ya anthu apatsa chakudya chochuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umu ndi mmene Iye amalamulira mitundu ya anthu ndi kuwapatsa chakudya chochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti aweruza nazo mitundu ya anthu. Apatsa cakudya cocuruka.