Job 36:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amagwira zing'aning'ani, ndipo amazilamula kuti zigwe pa malo amene Iye akufuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akutidwa manja ake ndi mphezi, nailamulira igwere pofunapo Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amadzaza manja ake ndi zingʼaningʼani, ndipo amazilamulira kuti zigwe pamalo pamene Iye akufuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akutidwa manja ace ndi mphezi, Nailamulira igwere pofunapo Iye.