Job 36:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kugunda kwake kumalengeza kuti Iye alipo, ndiye amalanga uchimo mwaukali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kugunda kwake kulalikira za Iye, zoweta zomwe zilota mtambo woyandikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabingu ake amalengeza za kubwera kwa mvula yamkuntho; ngʼombe nazo zimalengeza za kubwera kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kugunda kwace kulalikira za Iye, Zoweta zomwe zilota mtambo woyandikira.