Job 36:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, sindikunena zabodza. Wolankhula nanune ndine wanzeru kotheratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti zoonadi, mau anga sali abodza, wakudziwitsa mwangwiro ali nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithudi mawu anga si abodza; wanzeru zangwiro ali ndi inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti zoonadi, mau anga sali abodza, Wakudziwitsa mwangwiro ali nanu.