Job 36:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zoonadi, Mulungu ndi wamphamvu, sanyoza munthu aliyense, ndipo amadziŵa zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Mulungu ndiye mwini mphamvu, ndipo sapeputsa munthu; mphamvu ya nzeru zake ndi yaikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mulungu ndi wamphamvu, koma sanyoza anthu; Iye ndi wamphamvu, ndipo ndi wokhazikika pa cholinga chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Mulungu ndiye mwini mphamvu, ndipo sapeputsa munthu; Mphamvu ya nzeru zace ndi yaikuru.