Job 36:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Salola oipa kuti akhalebe ndi moyo, koma anthu osauka amaŵachitira zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sasunga woipa akhale ndi moyo, koma awaninkha ozunzika zowayenera iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salola oyipa kuti akhalebe ndi moyo koma amapereka ufulu kwa anthu osautsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sasunga woipa akhale ndi moyo, Koma awaninkha ozunzikazowayenera iwo.