Job 36:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo amatchinjiriza anthu opanda chifukwa, amalola kuti alamulire ngati mafumu, ndipo motero amalemekezeka mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sawachotsera wolungama maso ake, koma pamodzi ndi mafumu pa mpando wao awakhazika chikhazikire, ndipo akwezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye saleka kuyangʼanira anthu olungama; amawayika kuti alamulire pamodzi ndi mafumu ndipo amawalemekeza mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sawacotsera wolungama maso ace, Koma pamodzi ndi mafumu pa mpando wao Awakhazika cikhazikire, ndipo akwezeka.