Job 36:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu akamangidwa ndi nsinga, namazunzika chifukwa cha zimene adachita,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akamangidwa m'nsinga, nakakodwa ndi zingwe za mazunzo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati anthu amangidwa ndi unyolo, ndipo akondwa ndi zingwe zamasautso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akamangidwa m'nsinga, Nakakodwa ndi zingwe za mazunzo,