Job 36:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamenepo Mulungu amaŵasonyeza ntchito zao ndi zolakwa zao, kutsutsa kudzikuza kwao kochita kunyanya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo awafotokozera ntchito zao, ndi zolakwa zao, kuti anachita modzikuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amawafotokozera zomwe anachita, kuti iwo anachimwa modzikuza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo awafotokozera nchito zao, Ndi zolakwa zao, kuti anacita modzikuza.