Job 37:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanenso ndimaopa zazikuluzi, mtima wanga umalumphalumpha kuchoka m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa ichinso mtima wanga unjenjemera, nusunthika m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mtima wanga ukulumphalumpha pa chimenechinso ndipo ukuchoka mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa icinso mtima wanga unienjemera, Nusunthika m'malo mwace.