Job 37:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amayendetsa mitambo mozungulirazungulira, kuti ichite zonse zimene Iye akufuna pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo utembenukatembenuka pakulangiza kwake, kuti uchite zilizonse aulamulira, pa nkhope ya dziko lokhalamo anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amayendetsa mitamboyo mozungulirazungulira dziko lonse lapansi kuti ichite zonse zimene Iye akufuna pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo utembenuka-tembenuka pakulangiza kwace, Kuti ucite ziri zonse aulamulira, Pa nkhope ya dziko lokhalamo anthu;