Job 37:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwina amagwetsa mvula pansi pano kuti ikhale chilango, mwina kuti aonetse chikondi kwa anthu, pothirira nthaka yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati aufikitsira dziko lake kulidzudzula, kapena kulichitira chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amagwetsa mvula kuti alange anthu, kapena kubweretsa chinyontho pa dziko lapansi kuti aonetse chikondi chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati aufikitsira dziko lace kulidzudzula, Kapena kulicitira cifundo.