Job 37:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mukudziŵa m'mene Mulungu amazichitira, ndi m'mene amang'anipitsira mphezi m'mitambo yake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mudziwa umo Mulungu azilangizira zimenezi, nawalitsa mphezi ya m'mtambo mwake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mukudziwa momwe Mulungu amayendetsera mitambo ndi kuchititsa kuti kukhale zingʼaningʼani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mudziwa umo Mulungu azilangizira zimenezi, Nawalitsa mphezi ya m'mtambo mwace?