Job 37:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
paja inu zovala zanu mumamva kutentha kwambiri pamene mphepo yakumwera ikuwomba pa dziko?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mudziwa umo zovala zanu zifundira, pamene dziko lili thuu chifukwa cha mwera?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu amene mʼzovala zanu mumatuluka thukuta pamene kunja kwatentha chifukwa cha mphepo yakummwera,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mudziwa umo zobvala zanu zifundira, Pamene dziko liri thuu cifukwa ca mwela?