Job 37:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi nkofunikira kumdziŵitsa Mulungu kuti ndili naye ndi mau? Kodi kutero si kuchita ngati kupempha kuti ndiwonongeke?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi munthu ayenera kumuuza kuti ndifuna kunena, kapena kodi munthu adzakhumba kumezedwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi nʼkofunika kumudziwitsa Mulungu kuti ndili naye mawu? Kodi kutero sikuchita ngati kupempha kuti ndiwonongeke?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi munthu ayenera kumuuza kuti ndifuna kunena, Kapena kodi munthu adzakhumba kumezedwa?