Job 37:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsopano anthu sangathe kuyang'anitsitsa kuŵala, pamene kukunyezimira kwambiri mu mlengalenga, pamene mphepo yaomba nkuchotsa mitambo yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano anthu sakhoza kupenyerera kuunika pakunyezimira kuthambo, ndi mphepo yapita ndi kuuyeretsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano munthu sangathe kuyangʼana dzuwa, ndi kunyezimira mlengalenga, kuwomba kwa mphepo kutachotsa mitambo yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano anthu sakhoza kupenyerera kuunika pakunyezimira kuthambo, Ndi mphepo yapita ndi kuuyeretsa,