Job 37:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphambe sitingathe kumufika pafupi, ndi woopsa pa ulamuliro ndi pa mphamvu. Ndi wolungamadi kwambiri, sangazunze anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za Wamphamvuyonse, sitingamsanthule; ndiye wa mphamvu yoposa; koma mwa chiweruzo ndi chilungamo chochuluka samasautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wamphamvuzonse sitingathe kumufikira pafupi ndi wa mphamvu zoposa; pa chiweruzo chake cholungama ndi mʼchilungamo chake chachikulu Iye sapondereza anthu ozunzika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za Wamphamvuyonse, sitingamsanthule; ndiye wa mphamvu yoposa; Koma mwa ciweruzo ndi cilungamo cocuruka samasautsa.