Job 37:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake anthu amamuwopa kwambiri. Iye sasamalako wina aliyense amene amadzinyenga kuti ndi wanzeru.” Chauta alankhula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo anthu amuopa, Iye sasamalira aliyense wanzeru mumtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake anthu amamuopa kwambiri, kodi saganizira za onse amene amaganiza kuti ndi anzeru?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo anthu amuopa, Iye sasamalira ali yense wanzeru mumtima.