Job 37:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaponya ching'aning'ani pansi pa thambo, kuŵala kwake kumafika ku ngodya zonse za dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akumveketsa pansi pa thambo ponse, nang'anipitsa mphezi yake ku malekezero a dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amaponya chingʼaningʼani chake pansi pa thambo lonse ndipo amachitumiza ku dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akumveketsa pansi pa thambo ponse, Nang'anipitsa mphezi yace ku malekezero a dziko lapansi.