Job 37:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amachita zodabwitsa ndi liwu lake. Amachita zazikulu zimene sitingathe kumvetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu agunda modabwitsa ndi mau ake, achita zazikulu osazidziwa ife.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Liwu la Mulungu limabangula mʼnjira zambiri zodabwitsa Iye amachita zinthu zazikulu zimene sitingathe kuzimvetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu agunda modabwitsa ndi mau ace, Acita zazikuru osazidziwa ife.