Job 37:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalamula chisanu chambee kuti chigwe pa dziko lapansi. Amalamulanso mvula kuti igwe mwamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anena kwa chipale chofewa, Ugwe padziko, momwemonso kwa mvula, ndi kwa mvumbi waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amalamula chisanu chowundana kuti, ‘Igwa pa dziko lapansi,’ ndipo amalamulanso mvula yamawawa kuti, ‘Khala mvula yamphamvu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anena kwa cipale cofewa, Ugwe padziko. Momwemonso kwa mvula, Ndi kwa mbvumbi waukuru.