Job 37:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Mulungu amalepheretsa anthu kugwira ntchito zao. Motero iwowo amazindikira kuti Iye mwini ali pa ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atsekereza mokhomera chizindikiro dzanja la munthu aliyense, kuti anthu onse anawalenga adziwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuti anthu onse amene anawalenga athe kuzindikira ntchito yake. Iye amalepheretsa anthu kugwira ntchito zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atsekereza mokhomera cizindikilo dzanja la munthu ali yense, Kuti anthu onse anawalenga adziwe.