Job 39:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi iwe umaidziŵa nthaŵi imene zinkhoma zimaswera? Kodi udaziwonapo nswala zikubadwa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi udziwa nyengo yakuswana zinkhoma? Kodi wapenyerera pakuswa mbawala?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi iwe umadziwa nthawi imene mbalale yayikazi imaswera? Kodi umaonerera pamene nswala ikubala?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi udziwa nyengo yakuswana zinkhoma? Kodi wapenyerera pakuswa nswala?