Job 39:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungathe kuimanga ndi nsinga kuti izilima? Kodi ingasalaze nthumbira m'munda mwako?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ukhoza kumanga njati ndi lamba lake ilime m'mchera? Kapena idzakutsata kodi kufafaniza nthumbira m'zigwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ungathe kuyimanga ndi zingwe kuti izilima? Kodi ingasalaze nthumbira mʼmunda mwako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ukhoza kumanga njati ndi lamba lace ilime m'mcera? Kapena idzakutsata kodi kufafaniza nthumbira m'zigwa?